Yesaya 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pa nthawi imeneyo, Merodaki-baladani+ mwana wa Baladani mfumu ya Babulo,+ anatumiza makalata ndi mphatso+ kwa Hezekiya atamva kuti iye anadwala koma tsopano wapezanso mphamvu.+
39 Pa nthawi imeneyo, Merodaki-baladani+ mwana wa Baladani mfumu ya Babulo,+ anatumiza makalata ndi mphatso+ kwa Hezekiya atamva kuti iye anadwala koma tsopano wapezanso mphamvu.+