-
Yeremiya 19:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 ndiyeno ukawauze kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Mofanana ndi zimenezi, ndidzaswa anthu awa ndi mzinda uwu ngati mmene munthu amaswera botolo lopangidwa ndi woumba mbiya moti silingathe kukonzedwanso. Iwo adzaika maliro ku Tofeti mpaka sipadzapezekanso malo oika maliro kumeneko.”’+
-