-
Yeremiya 23:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 “Ine ndidzalanga aneneri amene akulota maloto abodza, amene akunena malotowo nʼkusocheretsa anthu anga chifukwa cha mabodza awo komanso kudzitama kwawo,” akutero Yehova.+
“Koma ine sindinawatume kapena kuwalamula kuti achite zimenezo. Choncho zochita zawo sizidzapindulitsa anthu awa ngakhale pangʼono,”+ akutero Yehova.
-