Yeremiya 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndidzawapatsa mtima woti andidziwe kuti ine ndine Yehova.+ Iwo adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo+ chifukwa adzabwerera kwa ine ndi mtima wawo wonse.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:7 Nsanja ya Olonda,3/15/2013, ptsa. 8-93/1/1994, ptsa. 14-15, 17
7 Ndidzawapatsa mtima woti andidziwe kuti ine ndine Yehova.+ Iwo adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo+ chifukwa adzabwerera kwa ine ndi mtima wawo wonse.+