Yeremiya 36:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ine ndidzaimba mlandu Yehoyakimu, ana ake* ndi atumiki ake chifukwa cha zolakwa zawo. Anthu amenewa komanso anthu amene akukhala mu Yerusalemu ndi mu Yuda ndidzawagwetsera masoka onse amene ndanena+ chifukwa sanamvere.’”’”+
31 Ine ndidzaimba mlandu Yehoyakimu, ana ake* ndi atumiki ake chifukwa cha zolakwa zawo. Anthu amenewa komanso anthu amene akukhala mu Yerusalemu ndi mu Yuda ndidzawagwetsera masoka onse amene ndanena+ chifukwa sanamvere.’”’”+