Yeremiya 44:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi mwaiwala zoipa zimene makolo anu, mafumu a Yuda+ komanso akazi awo ankachita?+ Kodi mwaiwala zinthu zoipa zimene inuyo ndi akazi anu+ munkachita mʼdziko la Yuda ndi mʼmisewu ya ku Yerusalemu?
9 Kodi mwaiwala zoipa zimene makolo anu, mafumu a Yuda+ komanso akazi awo ankachita?+ Kodi mwaiwala zinthu zoipa zimene inuyo ndi akazi anu+ munkachita mʼdziko la Yuda ndi mʼmisewu ya ku Yerusalemu?