Yeremiya 50:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu anga akhala ngati gulu la nkhosa zosochera.+ Abusa awo ndi amene anawasocheretsa.+ Anawatenga nʼkupita nawo mʼmapiri ndipo ankangowayendetsa kuchoka paphiri kupita pachitunda. Iwo aiwala malo awo opumulirako.
6 Anthu anga akhala ngati gulu la nkhosa zosochera.+ Abusa awo ndi amene anawasocheretsa.+ Anawatenga nʼkupita nawo mʼmapiri ndipo ankangowayendetsa kuchoka paphiri kupita pachitunda. Iwo aiwala malo awo opumulirako.