Maliro 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Achitira zachipongwe* akazi athu amene ali mʼZiyoni ndi anamwali amene ali mʼmizinda ya Yuda.+