Maliro 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Achitira zachipongwe+ akazi athu amene ali m’Ziyoni ndi anamwali amene ali m’mizinda ya Yuda.