Ezekieli 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, ukukhala pakati pa anthu opanduka. Maso ali nawo koma saona, makutu ali nawo koma samva+ chifukwa ndi anthu opanduka.+
2 “Iwe mwana wa munthu, ukukhala pakati pa anthu opanduka. Maso ali nawo koma saona, makutu ali nawo koma samva+ chifukwa ndi anthu opanduka.+