Ezekieli 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 ‘Pali ine Mulungu wamoyo,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ‘Ine ndidzakulamulirani monga mfumu yanu. Ndidzakulamulirani ndi dzanja lamphamvu, mkono wotambasula ndi mkwiyo wosefukira.+
33 ‘Pali ine Mulungu wamoyo,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ‘Ine ndidzakulamulirani monga mfumu yanu. Ndidzakulamulirani ndi dzanja lamphamvu, mkono wotambasula ndi mkwiyo wosefukira.+