Ezekieli 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “‘Pali ine Mulungu wamoyo,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ‘ndidzakhala mfumu yanu ndipo ndidzakulamulirani ndi dzanja lamphamvu, mkono wotambasula+ ndi mkwiyo wosefukira.+
33 “‘Pali ine Mulungu wamoyo,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ‘ndidzakhala mfumu yanu ndipo ndidzakulamulirani ndi dzanja lamphamvu, mkono wotambasula+ ndi mkwiyo wosefukira.+