Ezekieli 20:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kumeneko mudzakumbukira khalidwe lanu ndi zonse zomwe munkachita nʼkudziipitsa nazo+ ndipo mudzanyansidwa chifukwa cha zoipa zonse zimene munachita.+
43 Kumeneko mudzakumbukira khalidwe lanu ndi zonse zomwe munkachita nʼkudziipitsa nazo+ ndipo mudzanyansidwa chifukwa cha zoipa zonse zimene munachita.+