Ezekieli 20:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndithu kumeneko mudzakumbukira njira zanu+ ndi zochita zanu zonse zimene munali kudziipitsa nazo.+ Mukadzakumbukira zimenezi, mudzachita manyazi ochita kuonekera pankhope zanu chifukwa cha zoipa zonse zimene munachita.+
43 Ndithu kumeneko mudzakumbukira njira zanu+ ndi zochita zanu zonse zimene munali kudziipitsa nazo.+ Mukadzakumbukira zimenezi, mudzachita manyazi ochita kuonekera pankhope zanu chifukwa cha zoipa zonse zimene munachita.+