Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Chotero adzavomereza kuti iwo komanso makolo awo anayenda motsutsana nane,+ anandichimwira+ ndi kundichitira mosakhulupirika.

  • Nehemiya 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mukadzabwerera kwa ine+ ndi kusunga malamulo anga,+ ngakhale anthu omwazikana a mtundu wanu atakhala kumalekezero a kumwamba, ndidzawasonkhanitsa kuchokera kumeneko+ ndi kuwabweretsa+ kumalo amene ndasankha kuikako dzina langa.’+

  • Ezekieli 16:61
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 61 Ndithu udzakumbukira njira zako+ ndipo udzachita manyazi ukadzalandira akulu ako ndi ang’ono ako. Ndidzawapereka kwa iwe ngati ana ako aakazi,+ koma osati chifukwa cha pangano limene ndinapangana nawe.’+

  • Hoseya 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kenako ndidzabwerera kumalo anga kufikira iwo atalangidwa chifukwa cha zolakwa zawo+ ndipo adzayamba kufunafuna nkhope yanga.+ Zinthu zikadzawavuta,+ adzandifuna.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena