-
Ezekieli 27:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Chuma chako, katundu wako, malonda ako, anthu amene akukuyendetsa, anthu ako oyenda panyanja,
anthu omata molumikizira matabwa ako, anthu amene amakugulitsira malonda+ komanso asilikali ako onse,+
Gulu lonse la anthu amene ali mwa iwe,*
Onsewo adzamira pakati pa nyanja pa tsiku limene udzawonongedwe.+
-