13 Kenako anayeza kanyumba kapagetiko kuchokera padenga la chipinda chimodzi cha alonda kukafika padenga la chipinda china ndipo anapeza mikono 25. Khomo lililonse la chipinda cha alonda linali moyangʼanizana ndi khomo la chipinda cha mbali inayo.+