Ezekieli 40:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako ananditengera kumbali yakumʼmwera ndipo ndinaona kuti kumeneko kuli kanyumba kapageti kamene kanayangʼana kumʼmwera.+ Iye anayeza zipilala zake zamʼmbali ndi khonde lake ndipo miyezo yake inali yofanana ndi ya tinyumba tina tija.
24 Kenako ananditengera kumbali yakumʼmwera ndipo ndinaona kuti kumeneko kuli kanyumba kapageti kamene kanayangʼana kumʼmwera.+ Iye anayeza zipilala zake zamʼmbali ndi khonde lake ndipo miyezo yake inali yofanana ndi ya tinyumba tina tija.