Ezekieli 40:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kenako anandipititsa kugeti la kumpoto.+ Atayeza kanyumba kapagetiko, anapeza kuti miyezo yake inali yofanana ndi ya tinyumba tina tija.
35 Kenako anandipititsa kugeti la kumpoto.+ Atayeza kanyumba kapagetiko, anapeza kuti miyezo yake inali yofanana ndi ya tinyumba tina tija.