Ezekieli 40:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kenako ananditengera kuchipata cha kumpoto.+ Kumeneko iye anayeza kanyumba ka pachipatako ndipo miyezo yake inali yofanana ndi tinyumba tina tija.+
35 Kenako ananditengera kuchipata cha kumpoto.+ Kumeneko iye anayeza kanyumba ka pachipatako ndipo miyezo yake inali yofanana ndi tinyumba tina tija.+