Ezekieli 40:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Kumbali iliyonse ya khonde la kanyumba kapagetiko kunali matebulo awiri, pamene ankapherapo nsembe zopsereza zathunthu,+ nsembe zamachimo+ ndi nsembe zakupalamula.+
39 Kumbali iliyonse ya khonde la kanyumba kapagetiko kunali matebulo awiri, pamene ankapherapo nsembe zopsereza zathunthu,+ nsembe zamachimo+ ndi nsembe zakupalamula.+