Ezekieli 41:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako anayeza chipinda chimene chinayangʼanizana ndi malo oyera, ndipo anapeza kuti chinali mikono 20 mulitali ndi mikono 20 mulifupi.+ Ndiyeno anandiuza kuti: “Amenewa ndi Malo Oyera Koposa.”+
4 Kenako anayeza chipinda chimene chinayangʼanizana ndi malo oyera, ndipo anapeza kuti chinali mikono 20 mulitali ndi mikono 20 mulifupi.+ Ndiyeno anandiuza kuti: “Amenewa ndi Malo Oyera Koposa.”+