Ezekieli 41:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno anayeza makoma a chipinda chamkati kumbuyo kwa kachisi, ndipo anapeza kuti anali mikono 20 m’litali ndi mikono 20 m’lifupi.+ Kenako anandiuza kuti: “Amenewa ndi Malo Oyera Koposa.”+
4 Ndiyeno anayeza makoma a chipinda chamkati kumbuyo kwa kachisi, ndipo anapeza kuti anali mikono 20 m’litali ndi mikono 20 m’lifupi.+ Kenako anandiuza kuti: “Amenewa ndi Malo Oyera Koposa.”+