1 Mafumu 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chipinda chamkati chinali mikono 20 m’litali, mikono 20 m’lifupi+ ndi mikono 20 kutalika kwake. Chipindacho anachikuta ndi golide woyenga bwino,+ komanso anakuta guwa lansembe+ ndi matabwa a mkungudza. 2 Mbiri 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anapanga chipinda cha Malo Oyera Koposa.+ M’litali mwake chinali mikono 20+ mofanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Choncho m’lifupi mwake, chipindacho chinali mikono 20, ndipo anachikuta ndi golide wabwino wokwanira matalente* 600.
20 Chipinda chamkati chinali mikono 20 m’litali, mikono 20 m’lifupi+ ndi mikono 20 kutalika kwake. Chipindacho anachikuta ndi golide woyenga bwino,+ komanso anakuta guwa lansembe+ ndi matabwa a mkungudza.
8 Kenako anapanga chipinda cha Malo Oyera Koposa.+ M’litali mwake chinali mikono 20+ mofanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Choncho m’lifupi mwake, chipindacho chinali mikono 20, ndipo anachikuta ndi golide wabwino wokwanira matalente* 600.