15 Munthu uja anayeza kumbuyo kwa nyumba yomwe inayangʼanizana ndi malo opanda kanthu aja limodzi ndi timakonde take kumbali zonse ndipo anapeza kuti zinali mikono 100 mulitali.
Anayezanso Malo Oyera ndi Malo Oyera Koposa+ komanso makonde a bwalo,