2 Mbiri 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako iye anapanga chipinda cha Malo Oyera Koposa.+ Mulitali mwake chinali mikono 20 mofanana ndi mulifupi mwa nyumbayo ndipo mulifupi mwake chinali mikono 20. Anachikuta ndi golide wabwino wokwana matalente* 600.+ Ezekieli 41:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako anayeza chipinda chimene chinayangʼanizana ndi malo oyera, ndipo anapeza kuti chinali mikono 20 mulitali ndi mikono 20 mulifupi.+ Ndiyeno anandiuza kuti: “Amenewa ndi Malo Oyera Koposa.”+
8 Kenako iye anapanga chipinda cha Malo Oyera Koposa.+ Mulitali mwake chinali mikono 20 mofanana ndi mulifupi mwa nyumbayo ndipo mulifupi mwake chinali mikono 20. Anachikuta ndi golide wabwino wokwana matalente* 600.+
4 Kenako anayeza chipinda chimene chinayangʼanizana ndi malo oyera, ndipo anapeza kuti chinali mikono 20 mulitali ndi mikono 20 mulifupi.+ Ndiyeno anandiuza kuti: “Amenewa ndi Malo Oyera Koposa.”+