Zekariya 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Amuna ndi akazi achikulire adzakhalanso mʼmabwalo a mzinda wa Yerusalemu, aliyense atanyamula ndodo mʼmanja mwake chifukwa cha ukalamba.*+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:4 Nsanja ya Olonda,1/1/1996, ptsa. 11-16
4 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Amuna ndi akazi achikulire adzakhalanso mʼmabwalo a mzinda wa Yerusalemu, aliyense atanyamula ndodo mʼmanja mwake chifukwa cha ukalamba.*+