Zekariya 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘M’bwalo la mzinda wa Yerusalemu mudzakhala amuna ndi akazi achikulire.+ Aliyense adzatenga ndodo+ m’dzanja lake pakuti masiku ake adzakhala atachuluka. Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:4 Nsanja ya Olonda,1/1/1996, ptsa. 11-16
4 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘M’bwalo la mzinda wa Yerusalemu mudzakhala amuna ndi akazi achikulire.+ Aliyense adzatenga ndodo+ m’dzanja lake pakuti masiku ake adzakhala atachuluka.