Zekariya 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ‘Koma tsopano anthu anga otsala sindidzawachitiranso zinthu ngati mmene ndinachitira masiku akale,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
11 ‘Koma tsopano anthu anga otsala sindidzawachitiranso zinthu ngati mmene ndinachitira masiku akale,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.