Zekariya 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Anthu anga otsala sindidzawachitiranso zinthu ngati zimene ndinawachitira masiku akale,’+ watero Yehova wa makamu.
11 “‘Anthu anga otsala sindidzawachitiranso zinthu ngati zimene ndinawachitira masiku akale,’+ watero Yehova wa makamu.