Zekariya 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 A nyumba ya Efuraimu adzakhala ngati msilikali wamphamvu,Ndipo mumtima mwawo adzasangalala ngati amwa vinyo.+ Ana awo aamuna adzaona zimenezi ndipo adzakondwera.Mitima yawo idzakondwera chifukwa cha Yehova.+
7 A nyumba ya Efuraimu adzakhala ngati msilikali wamphamvu,Ndipo mumtima mwawo adzasangalala ngati amwa vinyo.+ Ana awo aamuna adzaona zimenezi ndipo adzakondwera.Mitima yawo idzakondwera chifukwa cha Yehova.+