7 chifukwa choti ndinaonetsedwa masomphenya apadera.
Koma kuti ndisadzikweze mopitirira malire, ndinapatsidwa minga mʼthupi+ mwanga imene imandibaya, imakhala ngati mngelo wa Satana ndipo imachititsa kuti ndizimva kuwawa nthawi zonse, nʼcholinga choti ndisadzikweze mopitirira malire.