2 Atesalonika 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pomaliza abale, pitirizani kutipempherera+ kuti mawu a Yehova* apitirize kufalikira mofulumira+ komanso kulemekezedwa ngati mmene akuchitira pakati panu. 2 Atesalonika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:1 Nsanja ya Olonda,1/15/1991, tsa. 23
3 Pomaliza abale, pitirizani kutipempherera+ kuti mawu a Yehova* apitirize kufalikira mofulumira+ komanso kulemekezedwa ngati mmene akuchitira pakati panu.