Aheberi 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mosiyana ndi akulu a ansembe ena, iye safunikira kupereka tsiku ndi tsiku nsembe+ za machimo ake choyamba, kenako za anthu ena.+ Zili choncho chifukwa iye anadzipereka kamodzi kokha kuti akhale nsembe yothandiza anthu mpaka kalekale.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:27 Nsanja ya Olonda,12/15/2008, ptsa. 14-15
27 Mosiyana ndi akulu a ansembe ena, iye safunikira kupereka tsiku ndi tsiku nsembe+ za machimo ake choyamba, kenako za anthu ena.+ Zili choncho chifukwa iye anadzipereka kamodzi kokha kuti akhale nsembe yothandiza anthu mpaka kalekale.+