Aheberi 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mmenemu munali chiwaya chagolide chofukizira nsembe+ ndi likasa la pangano+ lokutidwa ndi golide.+ Mulikasamo munali mtsuko wagolide wokhala ndi mana,+ ndodo ya Aroni imene inaphuka ija+ komanso miyala yosema+ ya pangano. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2144 Nsanja ya Olonda,1/15/2006, tsa. 31
4 Mmenemu munali chiwaya chagolide chofukizira nsembe+ ndi likasa la pangano+ lokutidwa ndi golide.+ Mulikasamo munali mtsuko wagolide wokhala ndi mana,+ ndodo ya Aroni imene inaphuka ija+ komanso miyala yosema+ ya pangano.