Aheberi 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komanso, wansembe aliyense amaima pamalo ake kuti achite utumiki wopatulika+ ndiponso kuti apereke nsembe zimodzimodzizo mobwerezabwereza,+ zimene sizingachotseretu machimo.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:11 Nsanja ya Olonda,11/15/2000, tsa. 11
11 Komanso, wansembe aliyense amaima pamalo ake kuti achite utumiki wopatulika+ ndiponso kuti apereke nsembe zimodzimodzizo mobwerezabwereza,+ zimene sizingachotseretu machimo.+