1 Petulo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho mukhale ndi chikhulupiriro cholimba ndipo mulimbane naye,+ podziwa kuti abale anu padziko lonse akukumananso ndi mavuto ngati omwewo.+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:9 Nsanja ya Olonda,5/15/2015, ptsa. 14-18
9 Choncho mukhale ndi chikhulupiriro cholimba ndipo mulimbane naye,+ podziwa kuti abale anu padziko lonse akukumananso ndi mavuto ngati omwewo.+