1 Petulo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma inu khalani olimba+ m’chikhulupiriro ndipo mulimbane naye, podziwa kuti anzanunso m’gulu lonse la abale anu m’dzikoli akukumana ndi masautso ngati omwewo.+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:9 Nsanja ya Olonda,5/15/2015, ptsa. 14-18
9 Koma inu khalani olimba+ m’chikhulupiriro ndipo mulimbane naye, podziwa kuti anzanunso m’gulu lonse la abale anu m’dzikoli akukumana ndi masautso ngati omwewo.+