1 Yohane 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi wabodza angakhalenso ndani kuposa amene amatsutsa kuti Yesu ndiye Khristu?+ Ameneyu ndi wokana Khristu,+ yemwe amakana Atate komanso Mwana. 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:22 Nsanja ya Olonda,6/1/2015, tsa. 14 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2137
22 Kodi wabodza angakhalenso ndani kuposa amene amatsutsa kuti Yesu ndiye Khristu?+ Ameneyu ndi wokana Khristu,+ yemwe amakana Atate komanso Mwana.