-
Chivumbulutso 2:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Taona! Ndatsala pangʼono kumudwalitsa kwambiri, ndipo amene akuchita naye chigololo ndiwabweretsera masautso aakulu, kupatulapo ngati atalapa ntchito zawo zofanana ndi za mayiyo.
-