-
Chivumbulutso 2:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Taona! Ndatsala pang’ono kumudwalitsa kwambiri, ndipo ochita naye chigololo ndiwaponya m’masautso aakulu, kupatulapo ngati atalapa ntchito zawo zofanana ndi za mayiyo.
-