Genesis 41:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Yosefe anali ndi zaka 30+ pamene anayamba kutumikira Farao, mfumu ya Iguputo. Kenako anachoka pamaso pa Farao n’kuyamba kuyendera dziko lonse la Iguputo. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:46 Nsanja ya Olonda,5/1/1987, tsa. 14
46 Yosefe anali ndi zaka 30+ pamene anayamba kutumikira Farao, mfumu ya Iguputo. Kenako anachoka pamaso pa Farao n’kuyamba kuyendera dziko lonse la Iguputo.