Numeri 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muwerenge kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ onse olowa m’gulu la ogwira ntchito+ m’chihema chokumanako. 2 Samueli 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Davide anali ndi zaka 30 pamene anakhala mfumu. Iye analamulira monga mfumu kwa zaka 40.+ Luka 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene Yesu anayamba ntchito yake,+ anali ndi zaka pafupifupi 30.+ Anthu ankakhulupirira kuti Yesu analimwana+ wa Yosefe,+mwana wa Heli,
3 Muwerenge kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ onse olowa m’gulu la ogwira ntchito+ m’chihema chokumanako.
23 Pamene Yesu anayamba ntchito yake,+ anali ndi zaka pafupifupi 30.+ Anthu ankakhulupirira kuti Yesu analimwana+ wa Yosefe,+mwana wa Heli,