Genesis 42:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano Yosefe ndiye anali wolamulira m’dzikomo.+ Iye ndiye anali kugulitsa tirigu kwa anthu onse ochokera kumayiko ena onse.+ Choncho abale a Yosefe anafika kwa iye. Anamugwadira n’kumuweramira mpaka nkhope zawo pansi.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:6 Nsanja ya Olonda,5/1/2015, tsa. 13
6 Tsopano Yosefe ndiye anali wolamulira m’dzikomo.+ Iye ndiye anali kugulitsa tirigu kwa anthu onse ochokera kumayiko ena onse.+ Choncho abale a Yosefe anafika kwa iye. Anamugwadira n’kumuweramira mpaka nkhope zawo pansi.+