7 Yehova Mulungu wakumwamba, amene ananditenga ine kunyumba kwa bambo anga ndi kudziko la abale anga,+ amenenso anandilankhula ndi kundilumbirira+ kuti, ‘Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbewu yako,’+ ameneyo atumiza mngelo wake kuti akutsogolere,+ ndipo kumeneko, ndithu ukam’tengere mwana wanga mkazi.+