-
Ekisodo 29:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Zimenezi zikhale za Aroni ndi ana ake mwa lamulo mpaka kalekale. Ana a Isiraeli ayenera kutsatira lamulo limeneli chifukwa ndi gawo lopatulika.+ Lidzakhala gawo lopatulika loyenera kuperekedwa ndi ana a Isiraeli. Limeneli ndi gawo lawo lopatulika loperekedwa kwa Yehova kuchokera pansembe zawo zachiyanjano.+
-