-
Ekisodo 29:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Zimenezi zikhale za Aroni ndi ana ake mwa lamulo mpaka kalekale. Aisiraeli ayenera kutsatira lamulo limeneli chifukwa ndi gawo lopatulika. Lidzakhala gawo lopatulika loyenera kuperekedwa ndi Aisiraeli.+ Limeneli ndi gawo lawo lopatulika loperekedwa kwa Yehova kuchokera pansembe zawo zamgwirizano.+
-