Ekisodo 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aroni azipaka ena mwa magazi a nyama ya nsembe yamachimo yophimbira machimo,+ panyanga za guwalo kuti aziphimbira machimo. Azichita zimenezi kamodzi pa chaka+ m’mibadwo yanu yonse. Kwa Yehova, guwalo ndi lopatulika koposa.”
10 Aroni azipaka ena mwa magazi a nyama ya nsembe yamachimo yophimbira machimo,+ panyanga za guwalo kuti aziphimbira machimo. Azichita zimenezi kamodzi pa chaka+ m’mibadwo yanu yonse. Kwa Yehova, guwalo ndi lopatulika koposa.”