Ekisodo 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aroni azipaka ena mwa magazi a nyama ya nsembe yamachimo panyanga za guwalo kuti aphimbe machimo+ a nyangazo. Azichita zimenezi kamodzi pa chaka+ mʼmibadwo yanu yonse. Kwa Yehova guwalo ndi lopatulika koposa.”
10 Aroni azipaka ena mwa magazi a nyama ya nsembe yamachimo panyanga za guwalo kuti aphimbe machimo+ a nyangazo. Azichita zimenezi kamodzi pa chaka+ mʼmibadwo yanu yonse. Kwa Yehova guwalo ndi lopatulika koposa.”