Ekisodo 40:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’chihemacho udzaikemonso tebulo+ ndi kuikapo zinthu zake mwadongosolo. Kenako udzaikemonso choikapo nyale+ ndi kuyatsa nyale zake.+
4 M’chihemacho udzaikemonso tebulo+ ndi kuikapo zinthu zake mwadongosolo. Kenako udzaikemonso choikapo nyale+ ndi kuyatsa nyale zake.+